Bungwe la Anti-Corruption Bureau likudziwitsa anthu onse kuti nambala ya ulere ya 113 yayambanso kugwira ntchito. Nambalayi ikugwira ntchito pa ma foni a netiweki ya TNM ndi Airtel.
Bungwe la ACB likulimbikitsa onse kugwiritsa ntchito nambalayi kupeleka madandaulo okhudzana ndi ziphuphu. Chonde tisagwiritse ntchito nambalayi pa zinthu zomwe sizikugwirizana ndi ntchito.
EGRITA M. NDALA
PRINCIPAL PUBLIC RELATIONS OFFICER
FOR: DIRECTOR GENERAL