ENGLISH VERSION
MALAWI MY MOTHERLAND
I pledge myself to my Malawi
To preserve her wealth and keep her beauty
To treat every citizen with respect
And enjoy my motherland
I’ll preserve the peace, I will break no law
I will take no bribe, live with love for all
To my Malawi I pledge myself My heart, my strength, my all
2. I’ll promote oneness, live in harmony
In my search for wealth seek integrity
In development I will give my best
Malawi my motherland
3. I’ll care for my land, keep Malawi clean
I will work hard for her prosperity
I will give myself to protect her name
And respect my motherland
CHICHEWA VERSION
MALAWI DZIKO LANGA
1. Ndadzipereka kwa Mayi Malawi
Kuteteza chuma kukongola kwake
Kulemekeza anthu onsewo
Kunyadira dziko langa
N’dzasunga bata ndi malamulo
N’dzapewa ziphuphu, kukonda anthu onse
Kwa Mayi Malawi ndadzipereka
Mtima wanga wonse
2. N’dzasunga umodzi ndi mgwirizano
N’dzapeza chuma mwa chilungamo
Pa chitukuko ndzadzipereka
Malawi dziko langa
3. Ndidzamsamala Malawi wanga
N’dzagwira ntchito modzipereka
Ndidzateteza, n’dzalemekeza
Malawi dziko langa
TUMBUKA VERSION
MALAWI CHARU CHANE
1. Nkhujipereka ku Malawi wane
Kusungilira chuma na Kutowa wake
Kupereka ntchindi ku waliyose
Nakuzaya na charu chane
Ndisunge mtende, ndiswe dango chara
Vimbundi nakana, nitemwe wose
Ku Malawi wane nkhujipereka
Ndamwene na vyane vyose
2. Nikwezgenge umoza kukhara mu mtende
Mukupenja chuma nichitenge urunji
Ku chitukuko nijipereke
Malawi charu chane
3. Nisungilire charu nakuchipwererera
Nijipereke kutukula charu
Nijipereke kuvikilira
Malawi charu chanega